ADVERTISEMENT
Mlatho Times
  • Home
  • News
    • All
    • Business
    • Crime
    • Culture
    • Politics
    • Religion
    • Tourism
    • World

    Tumbuka Chiefs to hold Chikulamayembe’s celebrations

    Nkhatabay legislator Vuwa Kaunda Chopped from DPP

    Police feigns ignorance on brutality during demos

    Two Behind Bars for theft of irrigation equipment

    Police Man hunt Chikwawa Chief’s murders

    Consortium to address violence against children held in Nsanje District

    Trending Tags

    • Market Stories
    • Election Results
  • Entertainment
    • All
    • Movie
    • Music
    • Sports

    Muyaba alavula moto pa kugonja kwa Moyale

    FAM Caught between horns on Kajoke

    FIFA funds Nsanje Stadium project.

    Malawi beach soccer team humbled by Mozambique.

    Hail!!Malawi’s Earling Haaland- “Muyaba”

    Nankhumwa tokens fundraising match with 1 million kwacha

  • Lifestyle
    • All
    • Fashion
    • Food
    • Health
    • Travel

    Nsanje Lalanje MP commends ESCOM for restoration of Transformer at Phokera Health Centre

    Teenage pregnancy rate worrisome -Activist

    Mask Off !!- Govt

    Malawi still registering Covid cases.

    Rumphi district wins fight against TB

    Kamoto Donating Blood

    Airtel partners MBTS in blood donation drive

    Trending Tags

    • Fashion Week
  • Columns

    Ntchisi Youth Office in “go back to school” campaign

    Rainford Kainga writes

    Stanley Onjezani Keneni writes:

    Trending Tags

    • Education

      Nsanje DC promises to be part of the school inspection team

      We Are One Malawi donates food items to children with disability

      Mbale Primary school faces tough challenges

      Chanco faces indefinite closure.

      UNIMA Student’s to go on pollls.

      Blantyre youths conduct Mussa parade

      Govt and Stakeholders urged to promote poetry in schools

      Education levels hit a snag in Chiladzulu

      MUST itsegulilidwa, atatseka kamba kazipolowe

      Trending Tags

      • Malawi Metro Music
      • The Bulletin
      ADVERTISEMENT
      No Result
      View All Result

          Home Entertainment

          Pemphero Mphande ndi ineyo tili pau bwenzi- Keturah

          Pomwe anthu ambiri atutumuka kuti chikuchitika ndi chani.

          Chaweya Mzembe by Chaweya Mzembe
          21 April 2022
          in Entertainment, Music, National, News
          0
          0
          SHARES
          93
          VIEWS
          Share on FacebookShare on TwitterShare on Whatsapp
          ADVERTISEMENT

          Mtsikana odziwika ndi luso lokalasa nsambo komanso kuimba chamba cha Afro-Pop kuno ku Malawi, Keturah, watsimikizira onse omutsatira kuti iye ali pa ubwenzi ndi Pemphero Mphande.
          Mu uthenga wake kudzera mu kanema ozijambula yekha yemwe wapereka kwa onse omutsata pa omutsatira lake la mchezo la Facebook mu usiku wa pa 20 April 2022, mtsikanayu anati wafuna kuwulula zoona zokhudza iye ndi Pemphero Mphande yemwe ndi m’modzi mwa anthu odziwika bwino pa tsamba la Facebook.

          “This is your local Girl Ketura, and I am here to tell you the truth about Pemphero Mphande, listen Pemphero Mphande and I are dating (Ine ndi ketura wanu wakomkuno kumudzi, ndipo ndili pano kuti ndikutsindikireni zoona zokhudza Pemphero Mphande. Tcherani philikanilo, Pemphero Mphande ndi ine tili pa Chibwezi ndithu),” anatsindika Ketura polankhula.
          Mawu a oyimbayu adza maka patamveka manong’onong’ono pa masamba a mchezo kuti awiriwa akhala akuzemberana zodziwika koma iwo amazemba kulankhulapo pa za izi.
          M’masiku apitawa, Pemphero Mphande yemwe adalinso omuongolera Keturah adati iye tsopano wasiya kukhalanso omuongolera m’mayimbidwe ake.
          Maganizo a anthu ena ati Keturah wadya mfulumila kulengeza za ubwenziwu, ndipo akadayembekeza kuti Pemphero Mphande ndiye akhale patsogolo kuvundukula ku gulu za ubwezi wawo wamseliwu.
          Pakadali pano, Mphande sadatsilirepo mlomo pa zomwe bwezi lake layankhula ku mtundu wa omukonda ndi kumutsata oyimbayu.
          Keturah ndi m’modzi mwa oyimba omwe ndi odziwika bwino m’Malawi maka kamba ka mawu ake a Nthetemya komanso luso lake lokalasa Nsambo lomwe adaphunzitsidwa ndi amalume ake m’mbuyomu. Iye wayimbapo nyimbo monga “Khalidwe ndi Chuma” komanso “Chembe”.

          Tags: KeturahPemphero mphande ndi bwenzi langa
          Chaweya Mzembe

          Chaweya Mzembe

          Stay Connected test

          • Trending
          • Comments
          • Latest

          MIA’S SECOND WIFE REJECTS K40M AS HER PART OF ESTATE BENEFIT

          9 May 2021

          Giddes Chalamanda given K2 million worth grocery store

          14 September 2020

          Presidential advisor Lucius Banda hospitalised

          5 January 2021

          Exam classes to get sample papers from MANEB

          15 September 2020

          CSOs lobby for Covid -19 internet reduction services

          1

          APM, JB must get matured – Analyst

          0

          25 year old man arrested for possessing cell phones without supporting documents

          0

          Polling Date not set – AG

          0

          Muyaba alavula moto pa kugonja kwa Moyale

          14 September 2023

          Tumbuka Chiefs to hold Chikulamayembe’s celebrations

          12 September 2023

          Analysts warns Chakwera’s persistent foreign travels

          12 September 2023

          Nkhatabay legislator Vuwa Kaunda Chopped from DPP

          8 September 2023

          Recent News

          Muyaba alavula moto pa kugonja kwa Moyale

          14 September 2023
          7

          Tumbuka Chiefs to hold Chikulamayembe’s celebrations

          12 September 2023
          10

          Analysts warns Chakwera’s persistent foreign travels

          12 September 2023
          8

          Nkhatabay legislator Vuwa Kaunda Chopped from DPP

          8 September 2023
          47

          Mlatho Times

          Mlatho Times

          We bring you the best news happening in Malawi and around the world.

          Follow Us

          Browse by Category

          • Agriculture
          • Business
          • Columns
          • Crime
          • Culture
          • Education
          • Entertainment
          • Environment
          • Fashion
          • Food
          • Health
          • International
          • Lifestyle
          • Malawi 2020 Elections
          • Malawi Art
          • Movie
          • Music
          • National
          • News
          • Opinion
          • Politics
          • Religion
          • Sports
          • Tourism
          • Travel
          • World

          Recent News

          Muyaba alavula moto pa kugonja kwa Moyale

          14 September 2023

          Tumbuka Chiefs to hold Chikulamayembe’s celebrations

          12 September 2023
          • Advertise with us
          • Contact Us

          © 2020 Mlatho Times - Website by Compufix Ltd.

          No Result
          View All Result
          • Home
          • National
          • Politics
          • Sports
          • Health
          • Travel
          • World
          • Columns
          • Education

          © 2020 Mlatho Times - Website by Compufix Ltd.