ADVERTISEMENT
Mlatho Times
  • Home
  • News
    • All
    • Business
    • Crime
    • Culture
    • Politics
    • Religion
    • Tourism
    • World

    Bangwe Police nab serial robbers

    A minor drawns in Lirangwe River in Chiradzulu

    MERA iyimitsa Kaye mikumano yake ndi a Malawi

    MultiChoice Malawi to challenge MACRA over tariffs

    Police officer arrested for allegedly shooting a minibus driver

    Angry residents broke in a warehouse over relief items

    Trending Tags

    • Market Stories
    • Election Results
  • Entertainment
    • All
    • Movie
    • Music
    • Sports

    FAM Caught between horns on Kajoke

    FIFA funds Nsanje Stadium project.

    Malawi beach soccer team humbled by Mozambique.

    Hail!!Malawi’s Earling Haaland- “Muyaba”

    Nankhumwa tokens fundraising match with 1 million kwacha

    Zambian football star Mwepu retires from cardiac arrest scare

  • Lifestyle
    • All
    • Fashion
    • Food
    • Health
    • Travel

    Nsanje Lalanje MP commends ESCOM for restoration of Transformer at Phokera Health Centre

    Teenage pregnancy rate worrisome -Activist

    Mask Off !!- Govt

    Malawi still registering Covid cases.

    Rumphi district wins fight against TB

    Kamoto Donating Blood

    Airtel partners MBTS in blood donation drive

    Trending Tags

    • Fashion Week
  • Columns

    Ntchisi Youth Office in “go back to school” campaign

    Rainford Kainga writes

    Stanley Onjezani Keneni writes:

    Trending Tags

    • Education

      Nsanje DC promises to be part of the school inspection team

      We Are One Malawi donates food items to children with disability

      Mbale Primary school faces tough challenges

      Chanco faces indefinite closure.

      UNIMA Student’s to go on pollls.

      Blantyre youths conduct Mussa parade

      Govt and Stakeholders urged to promote poetry in schools

      Education levels hit a snag in Chiladzulu

      MUST itsegulilidwa, atatseka kamba kazipolowe

      Trending Tags

      • Malawi Metro Music
      • The Bulletin
      ADVERTISEMENT
      No Result
      View All Result
      • Home
      • News
        • All
        • Business
        • Crime
        • Culture
        • Politics
        • Religion
        • Tourism
        • World

        Bangwe Police nab serial robbers

        A minor drawns in Lirangwe River in Chiradzulu

        MERA iyimitsa Kaye mikumano yake ndi a Malawi

        MultiChoice Malawi to challenge MACRA over tariffs

        Police officer arrested for allegedly shooting a minibus driver

        Angry residents broke in a warehouse over relief items

        Trending Tags

        • Market Stories
        • Election Results
      • Entertainment
        • All
        • Movie
        • Music
        • Sports

        FAM Caught between horns on Kajoke

        FIFA funds Nsanje Stadium project.

        Malawi beach soccer team humbled by Mozambique.

        Hail!!Malawi’s Earling Haaland- “Muyaba”

        Nankhumwa tokens fundraising match with 1 million kwacha

        Zambian football star Mwepu retires from cardiac arrest scare

      • Lifestyle
        • All
        • Fashion
        • Food
        • Health
        • Travel

        Nsanje Lalanje MP commends ESCOM for restoration of Transformer at Phokera Health Centre

        Teenage pregnancy rate worrisome -Activist

        Mask Off !!- Govt

        Malawi still registering Covid cases.

        Rumphi district wins fight against TB

        Kamoto Donating Blood

        Airtel partners MBTS in blood donation drive

        Trending Tags

        • Fashion Week
      • Columns

        Ntchisi Youth Office in “go back to school” campaign

        Rainford Kainga writes

        Stanley Onjezani Keneni writes:

        Trending Tags

        • Education

          Nsanje DC promises to be part of the school inspection team

          We Are One Malawi donates food items to children with disability

          Mbale Primary school faces tough challenges

          Chanco faces indefinite closure.

          UNIMA Student’s to go on pollls.

          Blantyre youths conduct Mussa parade

          Govt and Stakeholders urged to promote poetry in schools

          Education levels hit a snag in Chiladzulu

          MUST itsegulilidwa, atatseka kamba kazipolowe

          Trending Tags

          • Malawi Metro Music
          • The Bulletin
          No Result
          View All Result
          Mlatho Times
          No Result
          View All Result
          ADVERTISEMENT
          Home Lifestyle Health

          President Chakwera walimbikitsa nchito yolimbana ndi mlili wa Covid-19

          Chaweya Mzembe by Chaweya Mzembe
          2 February 2021
          in Health
          0
          0
          SHARES
          17
          VIEWS
          Share on FacebookShare on TwitterShare on Whatsapp

          Pulezidenti Lazarus Chakwera watsimikizira mtundu wa a Malawi kuti nkhondo yolimbana ndi nthenda ya covid-19 ikutheka tsiku ndi tsiku ndipo kuti boma lake liyesetsa kuti muliliwu utheretu mdziko muno.

          Polankhula mu uthenga wake ku mtundu wa Malawi kuchokera kunyumba ya boma ya Kamuzu mu mzinda wa Lilongwe Lamulungu lapitali pa Januwale 31, pulezidenti Chakwera mwa zina adati mwa anthu okwanira 17,334 omwe adayezedwa ngati ali ndi matenda a covid, anthu 5,027 okha ndamene adapezeka kuti ali ndi zizindikiro za matendawa, kuyimira anthu 29 mwa anthu 100 aliwonse omwe adayezedwa. Iye adati chiwerengerochi chatsika ndi anthu 8 pa 100 aliwonse poyaluzira msabata lapitalo pomwe anthu 37 mwa anthu 100 aliwonse adapezeka ndi kachirombo ka corona.

          Pulezidenti chakwera adaonjezera kunena kuti polimbikitsa ntchito yomenyana ndi covid-19 boma lake lakhazikitsa malo oyezeramo matendawa okwanira 62 pomwe akuyembekezera kuti akwane 77, zipangizo zoyezera zokwana 51,500 zagawidwa kale dziko lonse ndipo kuti zina zokwana 150,000 zikusungidwa pomwe zinanso zikuyembekezeka kufika mdziko muno posachedwapa.

          Mtsogoleri wadziko linoyu adapitilira mkulangiza mtundu wa a Malawi kuti nkhondoyi ikufunika kutsatira kwathunthu zitsogozo zomwe iye adakhazikitsa masabata apitawo ngati Malawi akufunitsitsa kupambana.

          ADVERTISEMENT

          Pa za katemera wa matenda a covid pulezidenti Chakwera adatsimikizira a Malawi kuti akatswiri azdzayenera kuwunika mozama asadayambe kupereka katemerayo kuti adzaone ngati kuli koyenera kupereka kapena ayi, koma pulezidenti Chakwera adatsimikiza kuti boma lake chikuchita chilichonse chotheka kuti mulili wa Covid-19 usapitilire kufala komanso kutenga miyoyo ya mzika za dziko lino, ndipo adathokonza magulu onse omwe akuthandizira kuti ntchito yolimbana ndi matendewa ikhale ya phindu mdziko muno.

          Mkulankhula kwawo a Chakwera sadanenepo kanthu ngati sukulu zomwe zinatsekedwa mongoyembekezera kamba kakufala kwa mulili wa covid zitsekulidweso posachedwapa kapena awonjezeraso nthawi ina pakutha pa masabata atatu omwe adalengeza kuti sukuluzi zikhale zotsekedwa.

          Tags: Chakweracovid-19 in Malawi
          Chaweya Mzembe

          Chaweya Mzembe

          Stay Connected test

          • Trending
          • Comments
          • Latest

          MIA’S SECOND WIFE REJECTS K40M AS HER PART OF ESTATE BENEFIT

          9 May 2021

          Giddes Chalamanda given K2 million worth grocery store

          14 September 2020

          Presidential advisor Lucius Banda hospitalised

          5 January 2021

          Exam classes to get sample papers from MANEB

          15 September 2020

          CSOs lobby for Covid -19 internet reduction services

          1

          APM, JB must get matured – Analyst

          0

          25 year old man arrested for possessing cell phones without supporting documents

          0

          Polling Date not set – AG

          0

          FAM Caught between horns on Kajoke

          26 May 2023

          Bangwe Police nab serial robbers

          17 May 2023

          A minor drawns in Lirangwe River in Chiradzulu

          1 March 2023

          Chaos in Parliament as Chakwera delivers SONA

          23 February 2023

          Recent News

          FAM Caught between horns on Kajoke

          26 May 2023
          4

          Bangwe Police nab serial robbers

          17 May 2023
          3

          A minor drawns in Lirangwe River in Chiradzulu

          1 March 2023
          7

          Chaos in Parliament as Chakwera delivers SONA

          23 February 2023
          8

          Mlatho Times

          Mlatho Times

          We bring you the best news happening in Malawi and around the world.

          Follow Us

          Browse by Category

          • Agriculture
          • Business
          • Columns
          • Crime
          • Culture
          • Education
          • Entertainment
          • Environment
          • Fashion
          • Food
          • Health
          • International
          • Lifestyle
          • Malawi 2020 Elections
          • Malawi Art
          • Movie
          • Music
          • National
          • News
          • Opinion
          • Politics
          • Religion
          • Sports
          • Tourism
          • Travel
          • World

          Recent News

          FAM Caught between horns on Kajoke

          26 May 2023

          Bangwe Police nab serial robbers

          17 May 2023
          • Advertise with us
          • Contact Us

          © 2020 Mlatho Times - Website by Compufix Ltd.

          No Result
          View All Result
          • Home
          • National
          • Politics
          • Sports
          • Health
          • Travel
          • World
          • Columns
          • Education

          © 2020 Mlatho Times - Website by Compufix Ltd.