ADVERTISEMENT
Malawi Metro News
ADVERTISEMENT
  • Home
  • News
    • All
    • Business
    • Crime
    • Culture
    • Politics
    • Religion
    • Tourism
    • World

    MERA iyimitsa Kaye mikumano yake ndi a Malawi

    MultiChoice Malawi to challenge MACRA over tariffs

    Police officer arrested for allegedly shooting a minibus driver

    Angry residents broke in a warehouse over relief items

    Ophunzila apha munthu pomuganizila kuti ndiwakuba

    14 years in Jail for round robbing a filling station

    Trending Tags

    • Market Stories
    • Election Results
  • Entertainment
    • All
    • Movie
    • Music
    • Sports

    FIFA funds Nsanje Stadium project.

    Malawi beach soccer team humbled by Mozambique.

    Hail!!Malawi’s Earling Haaland- “Muyaba”

    Nankhumwa tokens fundraising match with 1 million kwacha

    Zambian football star Mwepu retires from cardiac arrest scare

    Rumphi Utd itsanzika Mu TNM super league

  • Lifestyle
    • All
    • Fashion
    • Food
    • Health
    • Travel

    Nsanje Lalanje MP commends ESCOM for restoration of Transformer at Phokera Health Centre

    Teenage pregnancy rate worrisome -Activist

    Mask Off !!- Govt

    Malawi still registering Covid cases.

    Rumphi district wins fight against TB

    Kamoto Donating Blood

    Airtel partners MBTS in blood donation drive

    Trending Tags

    • Fashion Week
  • Columns

    Ntchisi Youth Office in “go back to school” campaign

    Rainford Kainga writes

    Stanley Onjezani Keneni writes:

    Trending Tags

    • Education

      Nsanje DC promises to be part of the school inspection team

      We Are One Malawi donates food items to children with disability

      Mbale Primary school faces tough challenges

      Chanco faces indefinite closure.

      UNIMA Student’s to go on pollls.

      Blantyre youths conduct Mussa parade

      Govt and Stakeholders urged to promote poetry in schools

      Education levels hit a snag in Chiladzulu

      MUST itsegulilidwa, atatseka kamba kazipolowe

      Trending Tags

      • Malawi Metro Music
      • The Bulletin
      No Result
      View All Result

          Home News Crime

          BANJA LAMANGIDWA PA MLANDU WOKUPHA MWANA

          Chaweya Mzembe by Chaweya Mzembe
          4 August 2020
          in Crime, National, News
          0
          2
          SHARES
          8
          VIEWS
          Share on FacebookShare on TwitterShare on Whatsapp

          Apolisi m’boma la Zomba amanga bambo Edson Peter a zaka 28 pamodzi ndi mkazi wawo a Esther Jonas a zaka 22 pa mlandu woti anapha mwana wawo wa mamuna wa zaka ziwiri (2) yemwe dzina lake ndi Evance Joseph yemwe anamwalira mu January 2020 mu mzinda wa Zomba.

          Bamboyo pamodzi ndi mkaziyo anakwatirana zaka ziwiri zapitazo ndipo bamboyo anapezeka mkaziyo ali ndi mwana kale (Evance Joseph) pa nthawi yomwe amkakwatilana.

          Mu January 2020, banjalo limkakhala ku Chilupya pomwe bamboyo amkapanga malonda ogulitsa tchipisi Pa 3 Miles.
          Tsiku lina bamboyo anafika ku nyumba usiku atagula botolo la mafuta ophikira, mwanayo yemwe ndi Evance Joseph amkasewera kenako anatenga botolo la mafuta ophikirawo koma mwa ngozi mafutawo anatayika zomwe zinapangitsa bamboyo kupsa mtima mpakana anamukakha mwanayo kumugwetsa pansi kuchokera pa nkhonde kenako mwanayo anakomoka koma bamboyo pamodzi ndi mkazi wakeyo anamusunga mwanayo m’nyumbamo osapita naye ku chipatala mpakana mwanayo anamwalira kenako bamboyo ndi mkaziyo anakumba dzenje ku munda wa chimanga komwe anakamukwilira mwanayo popanda kudziwitsa munthu aliyense za nkhaniyo.

          ADVERTISEMENT

          Bamboyo ndi mkaziyo amkanamiza anthu kuti mwanayo anamupititsa kwa agogo ake ku Mulanje kukacheza akhala kuti akufunsidwa mafunso ndi anthu okhuza kusowa kwa mwanayo kenako banjalo linachoka ku Chilupya ndikumakakhala ku Namikango trading centre.

          Pa 30 July 2020 bamboyo ndi mkaziyo anakangana mpakana mkaziyo anapita ku mudzi kwawo ku Mulanje koma atafundidwa mafunso okhuza za mwana wake uja iyeyo ananama kuti mwanayo ali ndi mamuna wake yemwe ndi bambo omupeza a mwana uja koma atamupanikiza ndi mafunso mzimayiyo anavomereza kuti mwanayo anamukwilira m’munda wa chimanga kenako mzimayiyo a Esther anamwa mankhwala kuti adzithe yekha pothawa mlandu wokupha koma sanamwalire Kamba koti anthu anamutengera ku chipatala mwa changu.

          Apolisi pa 3 July 2020 anamanga bamboyo pamodzi ndi mkazi wakeyo pa mlandu wokupha, kubisa imfa ya munthu, kukwilira munthu komanso mlandu wofuna kudzipha.

          Edson Peter amachokera m’mudzi mwa Sanjika T/A Kwataine m’boma la Ntcheu pomwe Esther Jonas amachokera m’mudzi mwa Kamoto T/A Mkanda m’boma la Mulanje.

          Tags: Murderzomba
          Chaweya Mzembe

          Chaweya Mzembe

          Stay Connected test

          • Trending
          • Comments
          • Latest

          MIA’S SECOND WIFE REJECTS K40M AS HER PART OF ESTATE BENEFIT

          9 May 2021

          Giddes Chalamanda given K2 million worth grocery store

          14 September 2020

          Presidential advisor Lucius Banda hospitalised

          5 January 2021

          Meet Catherine Phiri, Africa’s Rising Novelist

          15 June 2020

          CSOs lobby for Covid -19 internet reduction services

          1

          APM, JB must get matured – Analyst

          0

          25 year old man arrested for possessing cell phones without supporting documents

          0

          Polling Date not set – AG

          0

          MERA iyimitsa Kaye mikumano yake ndi a Malawi

          9 January 2023

          MultiChoice Malawi to challenge MACRA over tariffs

          9 January 2023

          Police officer arrested for allegedly shooting a minibus driver

          28 November 2022

          Angry residents broke in a warehouse over relief items

          25 November 2022

          Recent News

          MERA iyimitsa Kaye mikumano yake ndi a Malawi

          9 January 2023
          6

          MultiChoice Malawi to challenge MACRA over tariffs

          9 January 2023
          14

          Police officer arrested for allegedly shooting a minibus driver

          28 November 2022
          22

          Angry residents broke in a warehouse over relief items

          25 November 2022
          18

          Malawi Metro News

          Malawi Metro News

          Malawi Metro News

          We bring you the best news happening in Malawi and around the world.

          Malawi Metro News

          Follow Us

          Browse by Category

          • Agriculture
          • Business
          • Columns
          • Crime
          • Culture
          • Education
          • Entertainment
          • Environment
          • Fashion
          • Food
          • Health
          • International
          • Lifestyle
          • Malawi 2020 Elections
          • Malawi Art
          • Movie
          • Music
          • National
          • News
          • Opinion
          • Politics
          • Religion
          • Sports
          • Tourism
          • Travel
          • World

          Recent News

          MERA iyimitsa Kaye mikumano yake ndi a Malawi

          9 January 2023

          MultiChoice Malawi to challenge MACRA over tariffs

          9 January 2023
          • Advertise with us
          • Contact Us

          © 2020 Malawi Metro News - Website by Compufix Ltd.

          No Result
          View All Result
          • Home
          • National
          • Politics
          • Sports
          • Health
          • Travel
          • World
          • Columns
          • Education

          © 2020 Malawi Metro News - Website by Compufix Ltd.